Wednesday, 22 March 2017

Translators' Network International

Pastor Chris:Global Prayer Network.

NYANJA...
Mbusa Chris Global Prayer Network. Pempero pa 12 Koloko Zamdzuwa Ndi Teni Koloko Yausiku (Local/GMT) – Tsiku La Chitatu Kafukulira. Tinakhala pamodzi ndi Yesu kumwamba, ndipo Zintu zonse zili m’manja mwathu. Phunzirani zambiri mu Rhapsody ndipo yendelani kuchokera ku http://rhapsodyofrealities.org. Masalmo 103:1-5 ikuti “Lemekeza Yehova moyo wanga; ndi zonse za mkati mwanga zilemekeze dzina lace loyera. Lemekeza Yehova moyo wanga, ndi kusaiwala zokoma zace zonse aticitirazi: Amene akhululukira mphulupulu zaka zonse. Naciritsa nthenda zako zonse; Amene aombola moyo wako unganongeke: nakubveka korona wa cifundo ndi msoni zokoma. Amene akhutitsa m’kamwa mwako ndi zabwino nabweza ubwana wako unge mphungu.” Pa 12 koloko za mdzuwa ndi pa teni koloko za usiku mumzimu ndi kuyangana pa mau a Mulungu. Lekani mzimu oyera oyenda mu mitima yanu, cifundo ca Ambuye ndi chikondi cao chikhale pa inu nthawi zonse. Mupatseni mapembedzo. Hallelujah! Kumbukirani pakati pa mapempelo kupempera lero mu charichi.
for more info: www.kingsch.at

No comments:

Post a Comment